Ezekiel 23:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udatsanzira zochita za mkulu wako, ndipo ndidzaika chikho cha chilango chake m'manja mwako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wayenda m'njira ya mkulu wako, chifukwa chake ndidzapereka chikho chake m'dzanja lako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Unatsata zochita za mkulu wako; choncho Ine ndidzayika chikho cha chilango chake mʼdzanja lako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wayenda m'njira ya mkuru wako, cifukwa cace ndidzapereka cikho cace m'dzanja lako.