Ezekiel 23:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandifunsa kuti, “Iwe mwana wa munthu, kodi ukufuna kudzaweruza Ohola ndi Oholiba? Tsono uŵaimbe mlandu chifukwa cha zonyansa zao zimene adachita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, kodi udzaweruza Ohola ndi Oholiba? Uwafotokozere tsono zonyansa zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anandifunsa kuti, “Iwe mwana wa munthu, kodi udzaweruza Ohola ndi Oholiba? Tsono uwayimbe mlandu chifukwa cha machitidwe awo onyansa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, kodi udzaweruza Ohola ndi Oholiba? uwafotokozere tsono zonyansa zao.