Ezekiel 23:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachitanso izi: adaipitsa malo anga ondipembedzera, ndipo adanyoza masiku anga a Sabata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandichitiranso ichi, anadetsa malo anga opatulika tsiku lomwelo, naipsa masabata anga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anachitanso izi: Iwo anayipitsa malo anga opatulika ndi kudetsa masabata anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandicitiranso ici, anadetsa malo anga opatulika tsiku lomwelo naipsa masabata anga;