Ezekiel 23:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wamkulu anali Ohola, mng'ono wake anali Oholiba. Ndidaŵakwatira ndipo adandibalira ana aamuna ndi ana aakazi. ‘Ohola’ ndiye Samariya. ‘Oholiba’ ndiye Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo maina ao ndiwo Ohola wamkulu, ndi Oholiba mng'ono wake; nakhala anga, nabala ana aamuna ndi aakazi. Ndipo maina ao, Samariya ndiye Ohola, ndi Yerusalemu ndiye Oholiba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wamkulu dzina lake anali Ohola, ndipo mngʼono wakeyo anali Oholiba. Ine ndinawakwatira ndipo anabereka ana aamuna ndi ana aakazi. Ohola ndiye Samariya, ndipo Yerusalemu ndiye Oholiba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo maina ao ndiwo Ohola wamkuru, ndi Oholiba mng'ono wace; nakhala anga, nabala ana amuna ndi akazi. Ndipo maina ao, Samariya ndiye Ohola, ndi Yerusalemu ndiye Oholiba.