Ezekiel 23:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsiku lina anthu abwino adzaŵazenga anthuwo mlandu wa chigololo ndi wa kupha anzao. Zoonadi ngachigololo, ndipo m'manja mwao magazi ali psu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu olungama adzawaweruza monga mwa maweruzo a achigololo, ndi maweruzo akazi okhetsa mwazi; pakuti ndiwo achigololo, ndi m'manja mwao muli mwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu olungama adzawazenga anthuwa mlandu wa chigololo ndi wa kupha anthu. Ndi iwodi anthu achigololo ndiponso mʼmanja mwawo muli magazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu olungama adzawaweruza monga mwa maweruzo a acigololo, ndi maweruzo a akazi okhetsa mwazi; pakuti ndiwo acigololo, ndi m'manja mwao muli mwazi.