Ezekiel 23:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene ndikunena Ine Ambuye Chauta ndi izi: Itanani chigulu cha anthu, kuti chiŵazunze ndi kulanda chuma chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Ambuye Yehova, Ndidzawakweretsera msonkhano wa anthu, ndi kuwapereka awazunze, ndi kulanda chuma chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ambuye Yehova akuti: Itanitsani chigulu cha anthu kuti chidzawalange ndi kulanda chuma chawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Ambuye Yehova, Ndidzawakweretsera msonkhano wa anthu, ndi kuwapereka awazunze, ndi kulanda cuma cao.