Ezekiel 23:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akazi aŵiriwo aŵaponye miyala ndi kuŵatema ndi malupanga ao. Aphenso ana ao aamuna ndi aakazi ndipo atenthe nyumba zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi msonkhanowo udzawaponya miyala, ndi kuwatha ndi malupanga ao, adzawapha ana ao aamuna ndi aakazi, ndi kutentha nyumba zao ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthuwo adzawaponye miyala akazi awiriwo ndi kuwatema ndi malupanga awo. Ana awo aamuna ndi aakazi adzawaphe ndi kutentha nyumba zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi msonkhanowo udzawaponya miyala, ndi kuwatha ndi malupanga ao, adzawapha ana ao amuna ndi akazi, ndi kutentha nyumba zao ndi moto.