Ezekiel 23:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidzathetsa chiwerewere m'dziko lao, ndipo akazi onse adzaphunzira kuti asadzachite zonyansa ngati iwowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo ndidzaleketsa dama m'dzikomo, kuti alangizidwe akazi onse kusachita monga mwa dama lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Motero Ine ndidzathetsa zachigololo mʼdzikomo, ndipo akazi onse adzatengapo phunziro kuti asadzachite zachigololo monga za iwowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo ndidzaleketsa dama m'dzikomo, kuti alangizidwe akazi onse kusacita monga mwa dama lanu.