Ezekiel 23:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzalangidwa chifukwa cha makhalidwe ao achiwerewere, ndipo adzazunzika chifukwa cha tchimo la kupembedza mafano. Tsono adzadziŵa kuti Ine ndine Ambuye Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzakubwezerani dama lanu, nimudzasenza machimo a mafano anu; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawalanga chifukwa cha ntchito zawo za dama ndipo adzazunzika chifukwa cha tchimo lawo lopembedza mafano. Choncho adzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzakubwezerani dama lanu, nimudzasenza macimo a mafano anu; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.