Ezekiel 24:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma nkuuyeretsa bwanji? Dzimbiri lake lidaloŵerera, silingathe kuchoka ngakhale ndi moto womwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ntchito ya mphika ndi yolemetsa, koma dzimbiri lake lalikulu siliuchokera, dzimbiri lake liyenera kumoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mʼphikawo walephereka kuyeretsedwa. Dzimbiri lake linalowerera silingatheke kuchoka ngakhale ndi moto womwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nchito ya mphika ndi yolemetsa, koma dzimbiri lace lalikuru siliucokera, dzimbiri lace liyenera kumoto.