Ezekiel 24:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho ndidalankhula ndi anthu m'maŵa, madzulo mkazi wanga nkumamwalira. M'maŵa mwake, ndidachita monga momwe adandilamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo nditalankhula ndi anthu m'mawa, madzulo ake mkazi wanga anamwalira; ndi m'mawa mwake ndinachita monga anandilamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndinayankhula ndi anthu mmawa, ndipo madzulo mkazi wanga anamwalira. Mmawa mwake ndinachita monga momwe anandilamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo nditalankhula ndi anthu m'mawa, madzulo ace mkazi wanga anamwalira; ndi m'mawa mwace ndinacita monga anandilamulira.