Ezekiel 24:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, lemba dzina la tsiku lalero, lero lomwe lino. Lero ndilo tsiku limene mfumu ya ku Babiloni yazinga Yerusalemu ndi zithando zankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, Udzilembere dzina la tsiku lomwe lino, mfumu ya ku Babiloni wayandikira Yerusalemu tsiku lomwe lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu lemba dzina la tsiku lalero, lero lomwe lino, chifukwa mfumu ya Babuloni yazungulira Yerusalemu lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, Udzilembere dzina la tsiku lomwe lino, mfumu ya ku Babulo wayandikira Yerusalemu tsiku lomwe lino.