Ezekiel 24:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu mudzachita monga ndachitira inemu. Simudzaphimba kumaso, kapena kudya chakudya cha anthu olira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzachita monga umo ndachitira ine, osaphimba milomo yanu, kapena kudya mkate wa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mudzachita monga ndachitira inemu. Inu simudzaphimba nkhope zanu kapena kudya chakudya cha anamfedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzacita monga umo ndacitira ine, osaphimba milomo yanu, kapena kudya mkate wa anthu.