Ezekiel 24:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uŵaphere mwambi anthu aupanduŵa. Uŵauze kuti Ine Ambuye Chauta ndikuti, “ ‘Ikani mphika pa moto, ndipo muthiremo madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uphere nyumba yopandukayo fanizo, nunene nao, Atero Ambuye Yehova, Tereka mphika; uutereke, nuthire madzi m'menemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uwaphere mwambi anthu owukirawa ndi kuwawuza kuti: ‘Ambuye Yehova akuti, “ ‘Ikani mʼphika pa moto, ndipo mu mʼphikamo muthiremo madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uphere nyumba yopandukayo fanizo, nunene nao, Atero Ambuye Yehova, Tereka mphika; uutereke, nuthire madzi m'menemo.