Ezekiel 24:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magazi amene adakhetsa mumzindamo akadali pakati pake, chifukwa adaŵataya pa thanthwe losalala osati pa dothi, kuti fumbi lingaŵafotsere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwazi wake uli m'kati mwake anauika pathanthwe poyera, sanautsanulire panthaka kuukwirira ndi fumbi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Paja magazi amene anakhetsa akanali pakati pake mu mzindamo. Iye awakhuthulira pa thanthwe losalala. Sanawakhutulire pa dothi kuopa kuti fumbi lingawafotsere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwazi wace uli m'kati mwace anauika pathanthwe poyera, sanautsanulira panthaka kuukwirira ndi pfumbi.