Ezekiel 24:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaŵasiyadi magaziwo pa mwala wambee, kuti asafotsereke, chifukwa chofuna kuwonetsa mkwiyo wanga ndi kulipsira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pofuna kuutsa ukali, ndi kubwezera chilango, ndaika mwazi wake pathanthwe poyera, kuti usakwiririke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinasiya magaziwo pa mwala wosalala kuti asafotseredwe ndi fumbi chifukwa ndinafuna kuonetsa mkwiyo wanga ndi kulipsira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pofuna kuutsa ukali, ndi kubwezera cilango, ndaika mwazi wace pathanthwe poyera, kuti usakwiririke.