Ezekiel 25:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzapereka Amowabu pamodzi ndi Aamoni m'manja mwa mitundu yakuvuma, kotero kuti Aamoni adzaiŵalikiratu pakati pa mitundu ya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuwapereka kwa ana a kum'mawa pamodzi ndi ana a Amoni; ndipo ndidzawapereka akhale aoao, kuti ana a Amoni asakumbukikenso mwa amitundu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzapereka Amowabu pamodzi ndi Aamoni mʼmanja mwa anthu akummawa kotero kuti Aamoni adzayiwalikiratu pakati pa anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuwapereka kwa ana a kum'mawa pamodzi ndi ana a Amoni; ndipo ndidzawapereka akhale ao ao, kuti ana a Amoni asakumbukikenso mwa amitundu;