Ezekiel 25:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mau a Ine Ambuye Chauta ndi aŵa: Chifukwa choti Mowabu adanena kuti a ku Yuda ali ngati anthu ena onse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Popeza Mowabu ndi Seiri akuti, Taona nyumba ya Yuda ikunga amitundu onse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ambuye Yehova akuti, ‘Anthu a ku Mowabu ndi a ku Seiri ananena kuti anthu a ku Yuda ali ngati mayiko ena onse.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Popeza Moabu ndi Seiri akuti, Taona nyumba ya Yuda ikunga amitundu onse;