Ezekiel 25:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndidzagumula mbali ina ya Mowabu, ndidzaononga mizinda yake yakumalire, ndiye kuti mizinda ija yokongola kwambiriyi ya Beteyesimoti, Baala-Meyoni ndi Kiriyataimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake taona ndidzatsegula pambali pake pa Mowabu kuyambira kumidzi, kumidzi yake yokhala mphepete, yokometsetsa ya m'dziko, Beteyesimoti, Baala-Meoni, ndi Kiriyataimu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake ndidzagumula mbali ina ya Mowabu, kuyambira ku mizinda yake ya kumalire; mizinda yokongola ya Beti-Yesimoti, Baala-Meoni ndi Kiriataimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace taona, ndidzatsegula pambali pace pa Moabu kuyambira ku midzi, ku midzi yace yokhala mphepete, yokometsetsa ya m'dziko, Betiyesimoti, Baalameoni, ndi Kiriataimu,