Ezekiel 26:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka cha khumi ndi chimodzi cha ukapolo, tsiku loyamba la mwezi, Chauta adandipatsira uthenga uwu wakuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali chaka chakhumi ndi chimodzi, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chaka cha khumi ndi chimodzi, tsiku loyamba la mwezi, Yehova anandiyankhula kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali caka cakhumi ndi cimodzi, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,