Ezekiel 26:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene Ine Ambuye Chauta ndikukuuza iwe mzinda wa Tiro ndi izi: Nyanja idzagwedezeka pamodzi ndi zilumba, pakumva za kugwa kwako, ndiponso poona opweteka akubuula, ndipo anthu akuphedwa pakati pako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova kwa Tiro, Zisumbu sizidzagwedezeka nanga pomveka kugwa kwako, pobuula olasidwa, pakuchitika kuphako pakati pako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine Ambuye Yehova ndikukuwuza, iwe mzinda wa Turo, kuti zilumba zidzagwedezeka pakumva za kugwa kwako ndiponso poona anthu opweteka akubuwula ndipo anthu akuphedwa pakati pako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova kwa Turo, Zisumbu sizidzagwedezeka nanga pomveka kugwa kwako, pabuula olasidwa, pakucitika kuphako pakati pako?