Ezekiel 26:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano maiko a m'mbali mwa nyanja akunjenjemera chifukwa cha kugwa kwako. Nawonso okhala ku zilumba agwidwa ndi mantha chifukwa cha kutha kwako.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo zisumbu zidzanjenjemera tsiku la kugwa kwako, inde zisumbu za kunyanja zidzatenga nkhawa pa kuchokera kwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano mayiko a mʼmbali mwa nyanja akunjenjemera chifukwa cha kugwa kwako; okhala pa zilumba nawonso agwidwa ndi mantha aakulu chifukwa cha kugwa kwako.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo zisumbu zidzanjenjemera tsiku la kugwa kwako, inde zisumbu za kunyanja zidzatenga nkhawa pa kucokera kwako.