Ezekiel 26:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mau a Ine Ambuye Chauta ndi aŵa: Ndidzakusandutsa bwinja, ngati mzinda umene munthu sangathe kukhalamo. Ndidzakuphimba ndi madzi ozama am'nyanja, madzi amphamvu oti akumize.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Ambuye Yehova, Pamene ndikusandutsa mudzi wopasuka, ngati midzi yosakhalamo anthu, ndi kukukweretsera nyanja, nadzakumiza madzi aakulu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mawu a Ine Ambuye Yehova ndi awa: Ndidzakusandutsa bwinja, ngati mizinda imene anthu sangathe kukhalamo. Ndidzakuphimba ndi madzi ozama a mʼnyanja, madzi amphamvu woti akumize.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Ambuye Yehova, Pamene ndikusandutsa mudzi wapasuka, ngati midzi yosakhalamo anthu, ndi kukukweretsera nyanja, nadzakumiza madzi akuru;