Ezekiel 27:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu a ku Persiya, a ku Ludi ndi a ku Puti adaloŵa m'gulu la ankhondo ako. Ankapachika zishango zao ndi zisoti m'kati mwako, ndipo potero ankakupatsa ulemerero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apersiya, Aludi, Aputi, anali m'khamu lako; anthu ako a nkhondo anapachika chikopa ndi chisoti mwa iwe, anamveketsa kukoma kwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu a ku Perisiya, a ku Ludi ndi Puti anali asilikali mʼgulu lako la nkhondo. Iwo ankapachika zishango ndi zipewa zawo zankhondo pa makoma ako, kubweretsa kwa iwe ulemerero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aperisiya, Aludi, Apuri, anali m'khamu lako; anthu ako a nkhondo anapacika cikopa ndi cisoti mwa iwe, anamveketsa kukoma kwako.