Ezekiel 27:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, uimbe nyimbo yodandaulira Tiro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, Takwezera Tiro nyimbo ya maliro;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yodandaulira Turo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, Takwezera Turo nyimbo ya maliro;