Ezekiel 27:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Opalasa ako adakupititsa ku nyanja yozama, kumene mphepo yakuvuma idakukankhira nikumiza m'kati mwa nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Opalasa ako anakufikitsa kumadzi aakulu; mphepo ya kum'mawa inakuthyola m'kati mwa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu opalasa ako amakupititsa pa nyanja yozama. Koma mphepo yakummawa idzakuthyolathyola pakati pa nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Opalasa ako anakufikitsa ku madzi akuru; mphepo ya kum'mawa inakutyola m'kati mwa nyanja,