Ezekiel 27:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo akukulira iweyo, kulira kwake kwambiri. Akudzithira fumbi kumutu, nkumamvimvinizika pa phulusa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadzamveketsa mau ao pa iwe, nadzalira mowawa mtima, nadzathira fumbi pamitu pao, nadzakunkhulira m'maphulusa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo akufuwula, kukulira iwe kwambiri; akudzithira fumbi kumutu, ndi kudzigubuduza pa phulusa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nadzamveketsa mau ao pa iwe, nadzalira mowawa mtima, nadzathira pfumbi pamitu pao, nadzakunkhulira m'maphulusa,