Ezekiel 27:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akukuimbira nyimbo yodandaula, akuti, ‘Ndani adaonongedwapo ngati Tiro, pakati pa nyanja?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakulira adzakukwezera nyimbo ya maliro, ndi kukulirira, ndi kuti, Wakunga Tiro ndani, wakunga uyu waonongeka pakati pa nyanja?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuyimba nyimbo yokudandaulira nʼkumati: ‘Ndani anawonongedwapo ngati Turo pakati pa nyanja?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakulira adzakukwezera nyimbo ya maliro, ndi kukulirira, ndi kuti, Wakunga Turo ndani, wakunga uyu waonongeka pakati pa nyanja?