Ezekiel 27:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene malonda ako ankaoloka nyanja, unkakondweretsa mitundu yambiri ya anthu pa zosoŵa zao. Mafumu a dziko lapansi adalemera nacho chuma chako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutuluka malonda ako m'nyanja unadzaza mitundu yambiri ya anthu, unalemeretsa mafumu a pa dziko lapansi ndi chuma chako chochuluka ndi malonda ako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene malonda ako ankawoloka nyanja unakhutitsa mitundu yambiri ya anthu. Mafumu a dziko lapansi analemera ndi chuma chako komanso ndi malonda ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuturuka malonda ako m'nyanja unadzaza mitundu yambiri ya anthu, unalemeretsa mafumu a pa dziko lapansi ndi cuma cako cocuruka ndi malonda ako.