Ezekiel 27:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano wathyokera m'nyanja, pansi penipeni pa nyanja. Kungoti iweyo, katundu wako ndi antchito ako onse, nonse mwathera pamodzi m'nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muja unathyoka ndi nyanja m'madzi akuya malonda ako ndi msonkhano wako wonse adagwa pakati pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano wathyokera mʼnyanja, pansi penipeni pa nyanja. Katundu wako ndi onse amene anali nawe amira pamodzi nawe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muja unatyoka ndi nyanja m'madzi akuya malonda ako ndi msonkhano wako wonse adagwa pakati pako.