Ezekiel 27:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense amene amakhala m'mbali mwa nyanja waopsedwa nazo zimene zakuchitikira. Mafumu ao akuchita mantha, nkhope zao zasinthika ndi mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onse okhala pa zisumbu adagwa nawe, ndi mafumu ao aopsedwa kwambiri, zikhululuka nkhope zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse amene amakhala mʼmbali mwa nyanja aopsedwa ndi zimene zakuchitikira. Mafumu awo akuchita mantha ndipo nkhope zangoti khululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onse okhala pa zisumbu adagwa nawe, ndi mafumu ao aopsedwa kwambiri zikhululuka nkhope zao.