Ezekiel 27:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga nkhafi zako ndi mtengo wa thundu wa ku Basani. Adapanga thandala lako ndi matabwa a mitengo ya paini ya ku zilumba za Kitimu, pakati pa matabwawo panali zosema za minyanga ya njovu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anasema nkhafi zako za thundu wa ku Basani, anapanga mipando yako yamnyanga, woika mu mtengo wanaphini wochokera ku zisumbu za Kitimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mitengo ya thundu ya ku Basani anapanga zopalasira zako; ndi matabwa a mitengo ya payini yochokera ku zilumba za Kitimu. Pakuti anapanga thandala lako pakati pa matabwawo panali minyanga ya njovu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anasema nkhafi zako za thundu wa ku Basana, anapanga mipando yako yamnyanga, woika mu mtengo wanaphini wocokera ku zisumbu za Kitimu.