Ezekiel 28:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makhalidwe ako anali angwiro kuyambira tsiku limene udalengedwa mpaka nthaŵi imene udayamba kuchita zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Unali wangwiro m'njira zako chilengedwere iwe, mpaka chinapezeka mwa iwe chosalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makhalidwe ako anali abwino kuyambira pamene unalengedwa mpaka nthawi imene unayamba kuchita zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Unali wangwiro m'njira zako cilengedwere iwe, mpaka cinapezeka mwa iwe cosalungama.