Ezekiel 28:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mitundu yonse amene ankakudziŵa akuwopsedwa ndi zimene zidakuchitikira. Imfa yako inalidi yoopsa, ndipo sudzakhalanso mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onse akudziwa iwe mwa mitundu ya anthu adzadabwa nawe; wasanduka choopsa, ndipo sudzakhalanso konse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse amitundu amene ankakudziwa akuchita mantha chifukwa cha iwe. Watheratu mochititsa mantha ndipo sudzakhalaponso mpaka muyaya.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onse akudziwa iwe mwa mitundu ya anthu adzadabwa nawe; wasanduka coopsa, ndipo sudzakhalanso konse.