Ezekiel 28:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, utembenukire ku mzinda wa Sidoni ndipo ulose momdzudzula kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku Sidoni, nuunenere;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, utembenukire ku mzinda wa Sidoni ndipo unenere mowudzudzula kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku Zidoni, nuunenere;