Ezekiel 28:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Ine Ambuye Chauta ndikuti, Poti umadziganizira kuti ndiwe wanzeru ngati mulungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake atero Ambuye Yehova, Popeza waika mtima wako ngati mtima wa Mulungu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Choncho Ine Ambuye Yehova ndikuti, “ ‘Popeza umadziganizira kuti ndiwe mulungu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Popeza waika mtima wako ngati mtima wa Mulungu;