Ezekiel 29:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lakhumi ndi chiŵiri la mwezi wakhumi, chaka chakhumi cha ukapolo, Chauta adandipatsira uthenga uwu wakuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chakhumi, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi ndi chiwiri la mweziwo, anandidzera mau a Yehova, akuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lakhumi ndi chiwiri la mwezi wakhumi, chaka chakhumi, Yehova anandiyankhula kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cakhumi, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi ndi ciwiri la mweziwo, anandidzera mau a Yehova, akuti,