Ezekiel 29:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, chaka cha 27 cha ukapolo, Chauta adandipatsira uthenga uwu wakuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali chaka cha makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri mwezi woyamba, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, chaka cha 27, Yehova anandiyankhula kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri mwezi woyamba, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,