Ezekiel 29:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, umuimbe mlandu Farao, mfumu ya ku Ejipito, ndipo ulose modzudzula iyeyo pamodzi ndi dziko lake lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako itsutsane naye Farao mfumu ya Aejipito, nunenere motsutsana ndi iye, ndi Ejipito lonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, tembenukira kwa Farao, mfumu ya Igupto, ndipo unenere modzudzula mfumuyo pamodzi ndi dziko lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa: nkhope yako itsutsane naye Farao mfumu ya Aigupto, nunenere motsutsana ndi iye, ndi Aigupto lonse;