Ezekiel 29:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Motero onse okhala ku Ejipito adzadziŵa kuti Ine ndine Chauta. Iwe Ejipito unali ngati ndodo yabango kwa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi onse okhala m'Ejipito adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, popeza anakhalira nyumba ya Israele mchirikizo wabango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero aliyense amene amakhala mu Igupto adzadziwa kuti Ine ndine Yehova. “ ‘Iwe unakhala ngati ndodo yabango ku Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi onse okhala m'Aigupto adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, popeza anakhalira nyumba ya Israyeli mcirikizo wabango.