Ezekiel 3:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phokoso ndidaalimvalo linali la mapiko a zilengolengo zija akukhudzana mu mlengalenga, ndiponso phokoso la mikombero ya pambali pake ija, lomveka ngati chivomezi chachikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinamva mkokomo wa mapiko a zamoyozo pakukhudzana, ndi mlikiti wa njingazo m'mbali mwa izo, ndilo phokoso la mkokomo waukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Phokoso ndinkalimvalo linali la kugundana kwa mapiko a zamoyo ndiponso phokoso la mikombero ya pambali pake ija, limene linkamveka ngati chivomerezi chachikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinamva mkokomo wa mapiko a zamoyozo pakukhudzana, ndi mlikiti wa njingazo m'mbali mwa izo, ndilo phokoso la mkokomo waukuru.