Ezekiel 3:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma munthu woipa ukamchenjeza kuti asiye njira zake zoipa, iye nkumapitirizabe makhalidwe ake oipawo, adzafa ali ochimwa, Koma iweyo udzapulumutsa moyo wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ukachenjeza woipa, osabwerera iye kuleka choipa chake kapena njira yake yoipa, adzafa mu mphulupulu yake; koma iwe walanditsa moyo wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ukamuchenjeza munthu woyipa koma iye osatembenuka mtima kuleka zoyipa zake kapena kusiya njira zake zoyipa, munthuyo adzafa chifukwa cha uchimo wake koma iwe udzapulumutsa moyo wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ukacenjeza woipa, osabwerera iye kuleka coipa cace kapena njira yace yoipa, adzafa mu mphulupulu yace; koma iwe walanditsamoyo wako.