Ezekiel 3:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mzimu wa Mulungu udaloŵa mwa ine, ndipo udandiimiritsa. Apo Chauta adandilankhula nandiwuza kuti, “Pita kwanu, ukadzitsekere m'nyumba mwako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo unandilowa mzimu ndi kundiimika ndikhale chilili; ndipo analankhula ndi ine, nanena nane, Muka, katsekedwe m'nyumba mwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mzimu wa Mulungu unalowa mwa ine ndipo unandiyimiritsa. Tsono Yehova anandiyankhula nati: “Pita, kadzitsekere mʼnyumba mwako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo unandilowa mzimu ndi kundiimika ndikhale ciriri; ndipo analankhula ndi ine, nanena nane, Muka, katsekedwe m'nyumba mwako.