Ezekiel 3:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo kumeneko, iwe mwana wa munthu, adzakumanga ndi zingwe, kotero kuti sudzatha kuyendanso pakati pa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwe wobadwa ndi munthu, taona, adzakuikira iwe zingwe zolimba, nadzakumanga nazo, ndipo sudzatuluka pakati pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iwe mwana wa munthu, adzakumanga ndi zingwe motero kuti sudzatha kuyendanso pakati pa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwe wobadwa ndi munthu, taona, adzakuikira iwe zingwe zolimba, nadzakumanga nazo, ndipo sudzaturuka pakati pao;