Ezekiel 3:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakangamiza lilime lako kukhosi, kotero kuti sudzathanso kulankhula ndi kuŵachenjeza, chifukwa ndi anthu aupandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzamamatiritsa lilime lako kumalakalaka ako, kuti ukhale wosanena, wosawakhalira wakuwadzudzula; pakuti iwo ndiwo nyumba yopanduka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzamatirira lilime lako kukhosi, kotero kuti udzakhala chete wosatha kuwadzudzula, chifukwa iwo ndi anthu aupandu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzamamatiritsa lilime lako ku malakalaka ako, kuti ukhale wosanena, wosawakhalira wakuwadzudzula; pakuti iwo ndiwo nyumba yopanduka.