Ezekiel 3:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adandiwuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, pita kwa Aisraele, ukaŵauze mau anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, Muka, nufike kwa nyumba ya Israele, nunene nao mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Iye anandiwuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, pita tsopano kwa Aisraeli ndipo ukawawuze mawu anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, Muka, nufike kwa nyumba ya Israyeli, nunene nao mau anga.