Ezekiel 3:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindikukutuma kwa anthu olankhula chilankhulo chachilendo ndi chovuta ai, ndikukutuma kwa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sutumizidwa kwa anthu a chinenedwe chosamveka ndi chovuta, koma kwa nyumba ya Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sindikukutuma kwa anthu oyankhula chiyankhulo chachilendo ndi chovuta, koma kwa Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sutumizidwa kwa anthu a cinenedwe cosamveka ndi cobvuta, koma kwa nyumba ya Israyeli;