Ezekiel 30:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mau a Ine Ambuye Chauta ndi aŵa: Ndidzatuma Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni kuti adzathetse chuma cha Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Ndidzaleketsa kusokosera kwa Ejipito ndi dzanja la Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ine Ambuye Yehova ndikuti, “ ‘Ndidzagwiritsa ntchito Nebukadinezara, mfumu ya ku Babuloni kuti ndithetse gulu lankhondo la Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Ndidzaleketsa kusokosera kwa Aigupto ndi dzanja la Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo.