Ezekiel 30:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mzinda wa Patirosi ndidzausandutsa chipululu. Mzinda wa Zowani ndidzautentha. Mzinda wa Thebesi ndidzaulanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzasandutsa Patirosi labwinja, ndi kuika moto m'Zowani, ndi kukwaniritsa maweruzo m'No.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzasandutsa chipululu mzinda wa Patirosi, ndi kutentha mzinda wa Zowani. Ndidzalanga mzinda wa Thebesi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzasandutsa Patro labwinja, ndi kuika moto m'Zoani, ndi kukwaniritsa maweruzo m'No.