Ezekiel 30:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ejipito yense ndidzamtentha, ndipo Memfisi adzavutika kwambiri. Malinga a ku Thebesi adzagumuka, ndipo makoma ake adzaonongekeratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzaika moto m'Ejipito; Sini adzamva kuwawa kwakukulu, ndi No adzagawika pakati, ndi Nofu adzaona adani usana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzatentha ndi moto dziko la Igupto; Peluziumu adzazunzika ndi ululu. Malinga a Thebesi adzagumuka, ndipo mzindawo udzasefukira ndi madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzaika moto m'Aigupto; Sini adzamva kuwawa kwakukuru, ndi No adzagawika pakati, ndi Nofu adzaona adani usana.